Gawo 116
Zochokera mu Mbiri ya Joseph Smith zofotokoza vumbulutso loperekedwa kwa Joseph Smith Mneneri, pafupi ndi sitima ya Wight, pa malo otchedwa Spring Hill, Davies County, Missouri, Meyi kapena Juni 1838.
1Â Phiri la Spring litchulidwa ndi Ambuye kuti Adamu-ondi-Ahmani, chifukwa, iye adati, ndi malo amene Adamu adzabwera kudzayendera anthu ake, kapena Nkhalamba ya kale ya Masiku adzakhalapo, monga zidanenedwera ndi Daniel mneneri.