Nefi, mwana wa Helamani, atuluka mu mzindawo, ndipo mwana wake Nefi asunga zolemba—Ngakhale zizindikiro ndi zodabwitsa zidalipo zochuluka, oipa apanga dongosolo lokupha olungama—Usiku wa kubadwa kwa Khristu ufika—Chizindikiro chiperekedwa, ndipo nyenyezi yatsopano ituluka—Mabodza ndi chinyengo zichuluka, ndipo achifwamba a Gadiyantoni apha ambiri. Mdzaka dza pafupifupi Yesu atabadwa 1–4.