Mormoni atsogoleranso ankhondo Achinefi mu nkhondo za mwazi ndi kuphana—Buku la Mormoni lidzabwera kuti lidzatsimikizire Israeli yense kuti Yesu ndiye Khristu—Chifukwa cha kusakhulupilira kwawo, Alamani adzabalalika, ndipo Mzimu udzasiya kulimbana nawo—Iwo adzalandira uthenga wabwino kuchokera kwa Amitundu mu masiku otsiriza. Mdzaka dza pafupifupi Yesu atabadwa 375–384.